Langwan Piksy - Pakati Lyrics
VERSE ONEPakati, pa kuwala ndi mdimaPakati, pakutentha ndi kuziziraPakati, pa chubu ndi mpiraPakati, pa nkhuku ndi dziraNkakhala ofunda mudzandilavulaSinfuna kulavulidwaSinfuna kulavulidwaNdiri ngati munda wosalambulaNdifuna kupaliridwaNdifuna kupaliridwaCHORUSMundiike kumene mufunaMundiike kumene mufunaKuti zonse zomwe ndichitaZisangalatse inuMundiike kumene mufunaMundiike kumene mufunaKuti zonse zomwe ndichitaZisangalatse inuyoVERSE TWOPakati, pa mbuzi ndi gwapePakati, pa galu ndi nkhadwePakati, pa dzulo ndi leroPakati, pa usiwa ndi ulemeleroNkakhala ofunda mudzandilavulaSinfuna kulavulidwaSinfuna kulavulidwaNdiri ngati munda wosalambulaNdifuna kupaliridwaNdifuna kupaliridwaCHORUSMundiike kumene mufunaKumene mufunaKuti zonse zomwe ndichitaZisangalatse inuKumene mufunaMundiike kumene mufunaKuti zonse zomwe ndichitaZisangalatse inuyoVERSE THREESindziwa za mawaTsono ndikhala ndi nkhawaNdikhala moyo wa manthaNjira yanga iwunikidweOdziwa za ku mwambaAkuti ndiri nziwandaNdikhala moyo wa manthaNdingatani ndimasulidweNdingatani ndimasulidweNdiri pa katiiiiCHORUSMundiike kumene mufunaKumene mufunaKuti zonse zomwe ndichitaZisangalatse inuKumene mufunaMundiike kumene mufunaKuti zonse zomwe ndichitaZisangalatse inuyo