A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   E   »   Eminent Boiz Lyrics   »   Dosage Lyrics

Eminent Boiz - Dosage Lyrics

Font:      
Align:    
  • Verse 1
  • Kungodzuka mawa mami kufuna. ntakuonaaa
  • Nkona ndimabwera kwanu kusanache utha kuona
  • Chomwe ndimafuna Mami wekha sukudziwa
  • Koma chomwe ndimafuna mami ndekha ndimadziwa
  • Ndimataya ntima koma iwe sunditola
  • Kukusowa sindingathe poti nthawi sindilora
  • Tidadyetsana chani fanzi ati imangodabwa
  • Tima yoh tikakuyesa. tokhaso. kumangodabwa
  • Unaonamo. Mpaka lero simmadziwa
  • Ndilibe kalikose orso UNIMA anandisiya
  • Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa
  • Ena akuti overdose mu chikondi unandimiza
  • CHORUS(HOOK)
  • Iiineyooo
  • Kukhala opanda iwe sindigathe mami
  • Ndiwe doSage yanga
  • Umafunika nthawi yoyenerera
  • Without U sindimava bwino ineeeE
  • Ndiwe dossage yanga* X4
  • M'mawa masana madzulo ndiwe babie
  • Verse 2
  • Iweyo NDE kanyale sinkuthira madzi or manyowa
  • Zonse Unganena ndiku Mvera ngati Duwa
  • Ndilibe ntima mami ndiwe amene Nakupatsa
  • Ukatalikira ndimadanda ndekha ntangofatsa
  • Ndi. Dzafusira mbeta adzandirore kwanu komwe
  • Nsidzaopa kamulako ngati zamlomwe
  • Mawa masana Madzulo mami umafunikiraaa
  • Opanda iwe nditha kufa
  • Osamwinikila
  • Ati Chikondi pa chikondi imakhala nkhani ina
  • Nde Abatiya pa iweyo amapanga nkhani ina
  • Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa
  • Ena akuti overdose mu chikondi unandimiza
  • BACK TO HOOK
  • Verse 3
  • Ati swagg imandivuta ndinakhoza mpaka fail
  • Kodi tizinchonchonana? kukhala samatero
  • Amanena zambiri anthuwa ndimawamva
  • Koma sindiwatengera amavutika muntima
  • Ineyo opanda iwe na moyo umavuta
  • Ndiwe wanga wanga lady
  • Pamaso pa chauta
  • Dosage yokwanira sindipanga overdose
  • Ndikapanda kukuona ndimathakugwetsa Nsozi
  • Pamavuto pa ntendere mami
  • Umafunikira
  • Opanda iwe nditha kufa
  • Osapenekera
  • Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa
  • Ena akuti overdose muchikondi unandimiza

  • Report error in lyric




    Latest Eminent Boiz Lyrics

    The Dosage lyrics by Eminent Boiz is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
    Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
    You are now viewing Eminent Boiz Dosage Lyrics